814b955ace5c7f171ad837b2e2e2e67a.jpg

Nkhotakota - Bamba

Chionetsero chathu chomaliza pa Projecti yi chinatitengera ku malo otchedwa Bamba pa tsiku Lamulungu pa 23 October, 2022 ndipo kunali mpira pakati pa ma timu a mpira a Mthirah ndi Red Rangers, komanso mpira wa manja woti unasangalatsanso kwabasi.


Zithunzi

1 / 6
2 / 6
3 / 6
4 / 6
5 / 6
6 / 6

Hannah kukonzekera kuti ajambule zionetserozi ali pa denga la galimoto yokhulupirika ya mtundu wa Toyota Land Cruiser
Khamu likuyankha mafunso a kashembe ndikulandira ma t-sheti
Kutsata zionetsero ali pa denga la galimoto
Kukonzekera Mpira
Kukonzekera Mpira
Kutsanzikana kwa opanga Zionetsero