Pologram pa Waileyisi ya Umunthu pa 30 October 2022, Nkhotakota
Pologramu yapadera ya pa Wailesi ya Umunthu FM, yokamba za tizilombo ta kashembe, matenda a kashembe komanso Street Science pamene okambira ake anali a Gary Chilinga ndi Dr Jacob Kafulafula, ochokera ku Ofesi ya zaumoyo ya boma la Nkhotakota, Nkhotakota District Health Office.
< < Click for More